Numeri 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adzere m’dziko lake.+ M’malomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse n’kupita kukamenyana ndi Aisiraeli m’chipululumo. Anakafika ku Yahazi,+ kumene anayamba kumenyana ndi Aisiraeli. Nehemiya 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+
23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adzere m’dziko lake.+ M’malomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse n’kupita kukamenyana ndi Aisiraeli m’chipululumo. Anakafika ku Yahazi,+ kumene anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.
22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+