Deuteronomo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Hafu ya fuko la Manase ndinalipatsa dera lotsala la Giliyadi+ ndi Basana+ yense wa ufumu wa Ogi. Kodi si paja dera lonse la Arigobi+ limene ndi Basana yense, limatchedwa dziko la Arefai?+ Salimo 136:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anaphanso Ogi mfumu ya Basana:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
13 Hafu ya fuko la Manase ndinalipatsa dera lotsala la Giliyadi+ ndi Basana+ yense wa ufumu wa Ogi. Kodi si paja dera lonse la Arigobi+ limene ndi Basana yense, limatchedwa dziko la Arefai?+