Numeri 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pambuyo pake, anatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana.+ Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kukamenyana nawo pankhondo ya ku Edirei.+ Deuteronomo 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo Yehova adzachitira mitundu imeneyi zimene anachitira Sihoni+ ndi Ogi,+ mafumu a Aamori, ndiponso zimene anachitira dziko lawo, pamene anawawononga.+ Salimo 135:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+
33 Pambuyo pake, anatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana.+ Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kukamenyana nawo pankhondo ya ku Edirei.+
4 Ndipo Yehova adzachitira mitundu imeneyi zimene anachitira Sihoni+ ndi Ogi,+ mafumu a Aamori, ndiponso zimene anachitira dziko lawo, pamene anawawononga.+
11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+