Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+ Deuteronomo 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Zitatero, Yehova anandiuza kuti, ‘Taona, ndikupereka Sihoni ndi dziko lake kwa iwe. Yamba kulanda dziko lake.’+
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
31 “Zitatero, Yehova anandiuza kuti, ‘Taona, ndikupereka Sihoni ndi dziko lake kwa iwe. Yamba kulanda dziko lake.’+