Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+ Deuteronomo 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Zitatero, Yehova anandiuza kuti, ‘Taona, ndikupereka Sihoni ndi dziko lake kwa iwe. Yamba kulanda dziko lake.’+ Yoswa 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Pamapeto pake, ndinakufikitsani kudziko la Aamori amene anali kukhala kutsidya lina la Yorodano. Iwo anayamba kumenyana nanu,+ koma ine ndinawapereka m’manja mwanu kuti mutenge dziko lawo kukhala lanu. Chotero ndinawafafaniza kuwachotsa pamaso panu.+ Salimo 135:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
31 “Zitatero, Yehova anandiuza kuti, ‘Taona, ndikupereka Sihoni ndi dziko lake kwa iwe. Yamba kulanda dziko lake.’+
8 “‘Pamapeto pake, ndinakufikitsani kudziko la Aamori amene anali kukhala kutsidya lina la Yorodano. Iwo anayamba kumenyana nanu,+ koma ine ndinawapereka m’manja mwanu kuti mutenge dziko lawo kukhala lanu. Chotero ndinawafafaniza kuwachotsa pamaso panu.+
11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+