Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+

  • Deuteronomo 2:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Yehova Mulungu wathu anam’pereka kwa ife,+ ndipo tinam’gonjetsa+ limodzi ndi ana ake ndi anthu ake onse.

  • Yoswa 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano Mose anagawira dziko ana a Rubeni potsata mabanja awo.

  • Yoswa 13:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 mizinda yonse ya m’malo okwererapo,+ ndiponso dziko lonse la Sihoni mfumu ya Aamori imene inali kulamulira ili ku Hesiboni.+ Mfumu imeneyi Mose anaipha+ limodzi ndi atsogoleri a ku Midiyani, Evi, Rekemu, Zuri, Hura, ndi Reba.+ Amenewa anali mafumu omwe anali pansi pa Sihoni ndipo anali kukhala m’dzikolo.

  • Salimo 135:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+

      Ndi Ogi mfumu ya Basana,+

      Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena