Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+ Deuteronomo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno munafika pamalo ano, ndipo Sihoni mfumu ya Hesiboni+ ndi Ogi+ mfumu ya Basana anatuluka kudzamenyana nafe nkhondo, koma tinawagonjetsa.+
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
7 Ndiyeno munafika pamalo ano, ndipo Sihoni mfumu ya Hesiboni+ ndi Ogi+ mfumu ya Basana anatuluka kudzamenyana nafe nkhondo, koma tinawagonjetsa.+