Deuteronomo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova Mulungu wanu adzaupereka ndithu m’manja mwanu, ndipo zikatero muzipha mwamuna aliyense ndi lupanga.+ Nehemiya 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+ Salimo 135:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+ Salimo 136:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amenenso anapha mafumu olemekezeka:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
13 Yehova Mulungu wanu adzaupereka ndithu m’manja mwanu, ndipo zikatero muzipha mwamuna aliyense ndi lupanga.+
22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+
11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+ Salimo 136:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amenenso anapha mafumu olemekezeka:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
18 Amenenso anapha mafumu olemekezeka:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+