Deuteronomo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Yehova Mulungu wathu anaperekanso Ogi mfumu ya Basana ndi anthu ake onse m’manja mwathu, ndipo tinam’kantha moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka mwa anthu ake.+ Yoswa 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafukowa anatenganso dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali kulamulira ku Asitaroti ndi ku Edirei.+ Mfumu Ogi anali mmodzi mwa Arefai otsala.+ Mose anagonjetsa anthu onsewa ndi kuwapitikitsa.+
3 Pamenepo Yehova Mulungu wathu anaperekanso Ogi mfumu ya Basana ndi anthu ake onse m’manja mwathu, ndipo tinam’kantha moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka mwa anthu ake.+
12 Mafukowa anatenganso dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali kulamulira ku Asitaroti ndi ku Edirei.+ Mfumu Ogi anali mmodzi mwa Arefai otsala.+ Mose anagonjetsa anthu onsewa ndi kuwapitikitsa.+