33 Pambuyo pake, anatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana.+ Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kukamenyana nawo pankhondo ya ku Edirei.+
4 Pa nthawi imeneyo tinalanda mizinda yake yonse. Panalibe mzinda umene sitinawalande. Tinalanda mizinda 60+ m’chigawo chonse cha Arigobi,+ m’dera lonse la ufumu wa Ogi ku Basana.+