1 Mafumu 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi wake wa Solomo+ kuti: “Kodi simunamve kuti Adoniya mwana wa Hagiti+ wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakuzidziwa n’komwe zimenezi? 1 Mafumu 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano m’dzina la Yehova Mulungu wamoyo,+ amene wandichititsa kukhazikika,+ amene wandiika pampando wachifumu wa Davide bambo anga,+ ndiponso amene anandipatsa mzere wa banja lachifumu+ monga ananenera,+ lero Adoniya aphedwa.”+
11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi wake wa Solomo+ kuti: “Kodi simunamve kuti Adoniya mwana wa Hagiti+ wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakuzidziwa n’komwe zimenezi?
24 Tsopano m’dzina la Yehova Mulungu wamoyo,+ amene wandichititsa kukhazikika,+ amene wandiika pampando wachifumu wa Davide bambo anga,+ ndiponso amene anandipatsa mzere wa banja lachifumu+ monga ananenera,+ lero Adoniya aphedwa.”+