Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chonde, khululukani kulakwa kwa kapolo wanu wamkazi,+ pakuti mosalephera Yehova adzakukhazikitsirani nyumba yachifumu, inu mbuyanga, ndipo idzakhalapo kwa nthawi yaitali,+ chifukwa inu mbuyanga mukumenya nkhondo za Yehova.+ Ndipo mwa inu simudzapezeka choipa chilichonse masiku onse a moyo wanu.+

  • 2 Samueli 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 kuchokera tsiku limene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzakupatsa mpumulo kwa adani ako onse.+

      “‘“Tsopano Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira banja lachifumu.+

  • 1 Mbiri 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ngati mmene anachitira kuchokera masiku amene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndipo ndidzatsitsa adani ako onse.+ Tsopano ndikukuuza kuti: ‘Kuwonjezera pamenepo, Yehova adzakumangira nyumba.’*+

  • Salimo 127:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+

      Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+

      Yehova akapanda kulondera mzinda,+

      Alonda amakhala maso pachabe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena