Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Poyankha Davide anauza Mfilisitiyo kuti: “Iwe ukubwera kwa ine ndi lupanga, mkondo ndi nthungo,+ koma ine ndikubwera kwa iwe m’dzina la Yehova wa makamu,+ Mulungu wa asilikali a Isiraeli, amene iweyo wam’tonza.+

  • 1 Samueli 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno Sauli anauza Davide kuti: “Mwana wanga wamkazi wamkulu Merabu+ alipo. Ndidzakupatsa ameneyu kuti akhale mkazi wako.+ Koma iwe undisonyeze kulimba mtima kwako ndi kumenya nkhondo za Yehova.”+ Mumtima mwake Sauli anati: “Ndisamuphe ndine ndi dzanja langa, koma amuphe ndi Afilisiti.”+

  • 2 Samueli 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kuyambira kale+ pamene Sauli anali mfumu yathu, inuyo munali kutsogolera Isiraeli polowa ndi potuluka.+ Ndipo Yehova anakuuzani kuti, ‘Udzaweta+ anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri+ wa Isiraeli.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena