Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chotero ulamuliro wa Davide unakulirakulira,+ ndipo Yehova Mulungu wa makamu+ anali naye.+

  • 2 Samueli 22:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Mulungu woona ndiye malo anga otetezeka kwambiri,+

      Ndipo adzasalaza njira yanga.+

  • Salimo 44:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndi thandizo lanu tidzakankha adani athu.+

      M’dzina lanu tidzapondereza amene akutiukira.+

  • Salimo 125:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 125 Okhulupirira Yehova+

      Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+

  • Aheberi 11:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Anagonjetsa mphamvu ya moto,+ anathawa lupanga,+ anali ofooka koma anapatsidwa mphamvu,+ analimba mtima pa nkhondo,+ ndiponso anagonjetsa magulu ankhondo a mayiko ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena