Oweruza 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Samisoni+ anafuulira Yehova,+ kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, chonde, ndikumbukireni+ ndi kundipatsa mphamvu+ kamodzi kokhaka, inu Mulungu woona. Ndiloleni ndiwabwezere Afilisiti chifukwa cha limodzi mwa maso anga awiriwa.”+ 1 Mafumu 18:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+
28 Ndiyeno Samisoni+ anafuulira Yehova,+ kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, chonde, ndikumbukireni+ ndi kundipatsa mphamvu+ kamodzi kokhaka, inu Mulungu woona. Ndiloleni ndiwabwezere Afilisiti chifukwa cha limodzi mwa maso anga awiriwa.”+
46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+