Aheberi 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+
32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+