Oweruza 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero Afilisiti anam’gwira ndi kum’boola maso+ n’kupita naye ku Gaza.+ Anam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa,+ ndipo anakhala woyendetsa mwala wa mphero+ m’ndende.+ Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+ Salimo 143:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga muwakhalitse chete monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndipo muwononge onse ondichitira zoipa,+Pakuti ine ndine mtumiki wanu.+
21 Chotero Afilisiti anam’gwira ndi kum’boola maso+ n’kupita naye ku Gaza.+ Anam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa,+ ndipo anakhala woyendetsa mwala wa mphero+ m’ndende.+
10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+
12 Adani anga muwakhalitse chete monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndipo muwononge onse ondichitira zoipa,+Pakuti ine ndine mtumiki wanu.+