Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Patapita nthawi, Yehova anauza Samueli kuti: “Kodi ulirira Sauli+ mpaka liti, pamene ine ndamukana kuti alamulire monga mfumu ya Isiraeli?+ Thira mafuta m’nyanga yako+ ndipo unyamuke. Ndikutumiza kwa Jese+ wa ku Betelehemu, chifukwa ndapeza munthu pakati pa ana ake aamuna woti akhale mfumu yanga.”+

  • 2 Samueli 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pa nthawi yonse imene ndinali kuyendayenda pakati pa ana a Isiraeli onse,+ kodi ndinalankhulapo mawu ndi limodzi mwa mafuko onse a Isiraeli,+ fuko limene ndinalilamula kutsogolera anthu anga Aisiraeli, kuti, ‘N’chifukwa chiyani anthu inu simunandimangire nyumba ya mitengo ya mkungudza?’”’

  • Salimo 78:71
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+

      Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+

      Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena