2 Samueli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Izi zili choncho, Abineri analankhulana ndi akulu a Isiraeli kuti: “Kwa nthawi yaitali,+ mwakhala mukufuna Davide kuti akhale mfumu yanu.
17 Izi zili choncho, Abineri analankhulana ndi akulu a Isiraeli kuti: “Kwa nthawi yaitali,+ mwakhala mukufuna Davide kuti akhale mfumu yanu.