Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kuyambira kale+ pamene Sauli anali mfumu yathu, inuyo munali kutsogolera Isiraeli polowa ndi potuluka.+ Ndipo Yehova anakuuzani kuti, ‘Udzaweta+ anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri+ wa Isiraeli.’”

  • 1 Mbiri 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kuyambira kale, ngakhale pamene Sauli anali mfumu, inuyo munali kutsogolera Isiraeli polowa ndi potuluka.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu anakuuzani kuti, ‘Udzaweta+ anthu anga Aisiraeli, ndipo udzakhala mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena