Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiye zimene zidzachitika n’zakuti, chifukwa chakuti Yehova adzachitira inu mbuyanga zabwino zimene wanena kwa inu, iye adzakuikani kukhala mtsogoleri wa Isiraeli.+

  • 2 Samueli 6:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Poyankha, Davide anauza Mikala kuti: “Ine ndinali kusangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha kuti ndikhale mtsogoleri+ wa anthu a Yehova, Aisiraeli, m’malo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse, ndipo ndidzasangalala pamaso pa Yehova.+

  • 1 Mbiri 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena