1 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+ 1 Samueli 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anali kupita kwa Sauli ndi kubwerera ku Betelehemu kukaweta nkhosa+ za bambo ake. Salimo 78:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Choncho anasankha Davide mtumiki wake,+Ndipo anamuchotsa kumakola a nkhosa.+
12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+