1 Samueli 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiye zimene zidzachitika n’zakuti, chifukwa chakuti Yehova adzachitira inu mbuyanga zabwino zimene wanena kwa inu, iye adzakuikani kukhala mtsogoleri wa Isiraeli.+ 2 Samueli 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha, Davide anauza Mikala kuti: “Ine ndinali kusangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha kuti ndikhale mtsogoleri+ wa anthu a Yehova, Aisiraeli, m’malo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse, ndipo ndidzasangalala pamaso pa Yehova.+
30 Ndiye zimene zidzachitika n’zakuti, chifukwa chakuti Yehova adzachitira inu mbuyanga zabwino zimene wanena kwa inu, iye adzakuikani kukhala mtsogoleri wa Isiraeli.+
21 Poyankha, Davide anauza Mikala kuti: “Ine ndinali kusangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha kuti ndikhale mtsogoleri+ wa anthu a Yehova, Aisiraeli, m’malo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse, ndipo ndidzasangalala pamaso pa Yehova.+