Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo Sauli anati: “Amuna inu, mukauze Davide kuti, ‘Sikuti mfumu ikufuna ndalama za ukwati,+ koma ikufuna makungu 100 akunsonga + a Afilisiti, kuti ibwezere+ adani ake.’” Koma Sauli anali atakonza chiwembu kuti Davide aphedwe ndi Afilisiti.

  • 2 Samueli 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 M’kalatamo analembamo kuti:+ “Muike Uriya kutsogolo kumene nkhondo yakula,+ ndipo inu mubwerere m’mbuyo kuti amukanthe ndipo afe ndithu.”+

  • 2 Samueli 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni.

  • Salimo 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+

      Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena