Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni.

  • Salimo 51:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+

      Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+

  • Miyambo 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Usakonze zochitira mnzako choipa,+ pamene iye akuona kuti akukhala nawe mwamtendere.+

  • Miyambo 17:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Aliyense wobwezera zoipa pa zabwino,+ zoipa sizidzachoka panyumba pake.+

  • Zekariya 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Musamakonzerane ziwembu mumtima mwanu kuti muonetsane tsoka+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Pakuti zinthu zonsezi ine ndimadana nazo,’+ watero Yehova.”

  • Maliko 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti mkatimo, mumtima mwa munthu,+ mumatuluka maganizo oipa. Mumatuluka zadama,*+ zakuba, zaumbanda,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena