Zekariya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Chifukwa zinthu zonsezi ndimadana nazo,’+ watero Yehova.” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:17 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 20
17 Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Chifukwa zinthu zonsezi ndimadana nazo,’+ watero Yehova.”