Genesis 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamng’onoyu.”+ Genesis 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwezani kwambiri ndalama za ukwati ndi mphatso zoti ndipereke,+ ndipo ndine wokonzeka kupereka zilizonse zimene munganene, malinga mundipatse mtsikanayu kuti akhale mkazi wanga.” Ekisodo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Mwamuna akanyengerera namwali wosalonjezedwa kukwatiwa n’kugona naye,+ azim’tenga ndithu kukhala mkazi wake atapereka chiwongo.*+
18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamng’onoyu.”+
12 Kwezani kwambiri ndalama za ukwati ndi mphatso zoti ndipereke,+ ndipo ndine wokonzeka kupereka zilizonse zimene munganene, malinga mundipatse mtsikanayu kuti akhale mkazi wanga.”
16 “Mwamuna akanyengerera namwali wosalonjezedwa kukwatiwa n’kugona naye,+ azim’tenga ndithu kukhala mkazi wake atapereka chiwongo.*+