Genesis 31:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zonse pamodzi ndakhala zaka 20 m’nyumba mwanu. Ndakugwirirani ntchito zaka 14, kugwirira ana anu aakazi awiriwa. Zaka zinanso 6, ndagwirira ntchito ziweto. Koma inu munapitiriza kusinthasintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+ Genesis 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwezani kwambiri ndalama za ukwati ndi mphatso zoti ndipereke,+ ndipo ndine wokonzeka kupereka zilizonse zimene munganene, malinga mundipatse mtsikanayu kuti akhale mkazi wanga.”
41 Zonse pamodzi ndakhala zaka 20 m’nyumba mwanu. Ndakugwirirani ntchito zaka 14, kugwirira ana anu aakazi awiriwa. Zaka zinanso 6, ndagwirira ntchito ziweto. Koma inu munapitiriza kusinthasintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+
12 Kwezani kwambiri ndalama za ukwati ndi mphatso zoti ndipereke,+ ndipo ndine wokonzeka kupereka zilizonse zimene munganene, malinga mundipatse mtsikanayu kuti akhale mkazi wanga.”