Genesis 24:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kenako, mtumikiyo anayamba kutulutsa zinthu zasiliva, zagolide, ndi zovala n’kupatsa Rabeka. Anaperekanso zinthu zamtengo wapatali kwa mlongo wake wa Rabeka ndi kwa mayi ake.+ 1 Samueli 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Sauli anati: “Amuna inu, mukauze Davide kuti, ‘Sikuti mfumu ikufuna ndalama za ukwati,+ koma ikufuna makungu 100 akunsonga + a Afilisiti, kuti ibwezere+ adani ake.’” Koma Sauli anali atakonza chiwembu kuti Davide aphedwe ndi Afilisiti. Hoseya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero ndinagula mkaziyo ndi ndalama zasiliva 15+ ndi balere wokwana muyezo umodzi wa homeri* ndi hafu.
53 Kenako, mtumikiyo anayamba kutulutsa zinthu zasiliva, zagolide, ndi zovala n’kupatsa Rabeka. Anaperekanso zinthu zamtengo wapatali kwa mlongo wake wa Rabeka ndi kwa mayi ake.+
25 Pamenepo Sauli anati: “Amuna inu, mukauze Davide kuti, ‘Sikuti mfumu ikufuna ndalama za ukwati,+ koma ikufuna makungu 100 akunsonga + a Afilisiti, kuti ibwezere+ adani ake.’” Koma Sauli anali atakonza chiwembu kuti Davide aphedwe ndi Afilisiti.
2 Chotero ndinagula mkaziyo ndi ndalama zasiliva 15+ ndi balere wokwana muyezo umodzi wa homeri* ndi hafu.