2 Samueli 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuchokera tsiku limene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzakupatsa mpumulo kwa adani ako onse.+ “‘“Tsopano Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira banja lachifumu.+ Miyambo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uzim’kumbukira m’njira zako zonse,+ ndipo iye adzawongola njira zako.+ Mateyu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu+ wanu ubwere. Chifuniro chanu+ chichitike, monga kumwamba, chimodzimodzinso pansi pano.+ Aheberi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anali wokhulupirika+ kwa Mulungu amene anamuika kukhala mtumwi ndi mkulu wa ansembe, monga mmenenso Mose+ analili wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu.+ Yakobo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+
11 kuchokera tsiku limene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzakupatsa mpumulo kwa adani ako onse.+ “‘“Tsopano Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira banja lachifumu.+
2 Iye anali wokhulupirika+ kwa Mulungu amene anamuika kukhala mtumwi ndi mkulu wa ansembe, monga mmenenso Mose+ analili wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu.+
15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+