Miyambo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa,+ ndipo sawonjezerapo ululu.+ 1 Akorinto 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndife antchito anzake a Mulungu.+ Inuyo ndinu munda wa Mulungu umene ukulimidwa,+ nyumba ya Mulungu.+
9 Pakuti ndife antchito anzake a Mulungu.+ Inuyo ndinu munda wa Mulungu umene ukulimidwa,+ nyumba ya Mulungu.+