Oweruza 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+ Salimo 121:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova akukuyang’anira.+Yehova ndiye mthunzi wako+ kudzanja lako lamanja.+ Yesaya 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine Yehova ndine mlonda wa mundawo.+ Ndizidzauthirira nthawi zonse.+ Ndizidzaulondera usana ndi usiku kuti wina aliyense asauwononge.+ Zekariya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzamuzungulira ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ndidzamudzaza ndi ulemerero wanga,”’ watero Yehova.”+
8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+
3 Ine Yehova ndine mlonda wa mundawo.+ Ndizidzauthirira nthawi zonse.+ Ndizidzaulondera usana ndi usiku kuti wina aliyense asauwononge.+
5 Ine ndidzamuzungulira ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ndidzamudzaza ndi ulemerero wanga,”’ watero Yehova.”+