Miyambo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pereka ntchito zako kwa Yehova,+ ndipo zolinga zako ndithu zidzakhazikika.+ Yesaya 62:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+ Yeremiya 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwezerani mpanda wa Babulo mtengo wa chizindikiro.+ Wonjezerani alonda+ ndipo ikani alondawo pamalo awo. Konzekeretsani omenya nkhondo mobisalira anzawo.+ Pakuti Yehova waganiza zoti achite ndipo adzachitira anthu okhala ku Babulo zimene wanena.”+ Ezekieli 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi anthu a mtundu wako+ ndipo uwauze kuti,“‘Ndikabweretsa lupanga m’dziko,+ ndipo mogwirizana anthu a m’dzikolo akasankha munthu kuti akhale mlonda wawo,+
6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+
12 Kwezerani mpanda wa Babulo mtengo wa chizindikiro.+ Wonjezerani alonda+ ndipo ikani alondawo pamalo awo. Konzekeretsani omenya nkhondo mobisalira anzawo.+ Pakuti Yehova waganiza zoti achite ndipo adzachitira anthu okhala ku Babulo zimene wanena.”+
2 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi anthu a mtundu wako+ ndipo uwauze kuti,“‘Ndikabweretsa lupanga m’dziko,+ ndipo mogwirizana anthu a m’dzikolo akasankha munthu kuti akhale mlonda wawo,+