Nahumu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Womwaza wafika pamaso pako.+ Teteza malo amene ali ndi mpanda wolimba kwambiri. Londera njira yako. Konzekera kumenya nkhondo.* Kunga mphamvu zako zonse.+
2 Womwaza wafika pamaso pako.+ Teteza malo amene ali ndi mpanda wolimba kwambiri. Londera njira yako. Konzekera kumenya nkhondo.* Kunga mphamvu zako zonse.+