Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ndikuitana mafuko onse akumpoto,”+ watero Yehova, “ndipo ndikuitananso Nebukadirezara mfumu ya Babulo, mtumiki wanga.+ Ndikuitana anthu amenewa kuti aukire dziko lino+ ndi anthu okhala mmenemo, komanso kuti aukire mitundu yonse yokuzungulirani.+ Ndidzakuwonongani inuyo ndi mitundu yonse yokuzungulirani, ndi kukusandutsani chinthu chodabwitsa chimene azidzachiimbira mluzu+ ndipo malo anu adzakhala mabwinja mpaka kalekale.+

  • Yeremiya 49:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ngamila zawo+ zidzafunkhidwa ndipo ziweto zawo zochulukazo zidzawonongedwa. Anthu amene amadulira ndevu zawo za m’mbali+ ndidzawabalalitsira kumbali zonse.*+ Ndidzawagwetsera tsoka kuchokera kumadera onse owazungulira,” watero Yehova.

  • Ezekieli 29:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Dziko la Iguputo ndidzalisandutsa bwinja pakati pa mayiko omwe simukukhalanso anthu.+ Kwa zaka 40, mizinda yake idzakhala mabwinja pakati pa mizinda yopanda anthu.+ Ndidzamwaza Aiguputo pakati pa anthu a mitundu ina ndi kuwabalalitsira m’mayiko ena.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena