Yeremiya 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzasandutsa mzindawu kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena, chimene azidzachiimbira mluzu.+ Aliyense wodutsa pafupi nawo adzauyang’anitsitsa modabwa ndipo adzaulizira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+
8 Ndidzasandutsa mzindawu kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena, chimene azidzachiimbira mluzu.+ Aliyense wodutsa pafupi nawo adzauyang’anitsitsa modabwa ndipo adzaulizira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+