Yeremiya 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mzindawu ndidzausandutsa chinthu chochititsa mantha komanso chimene anthu azidzachiimbira mluzu. Aliyense wodutsa pafupi ndi mzindawo adzauyangʼanitsitsa mwamantha ndipo adzauimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+
8 Mzindawu ndidzausandutsa chinthu chochititsa mantha komanso chimene anthu azidzachiimbira mluzu. Aliyense wodutsa pafupi ndi mzindawo adzauyangʼanitsitsa mwamantha ndipo adzauimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+