Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kuwonjezera pamenepo, Solomo anaika magulu+ a ansembe pa utumiki wawo mogwirizana ndi lamulo la Davide bambo ake.+ Anaikanso Alevi+ pamalo awo a ntchito kuti azitamanda+ ndi kutumikira+ pamaso pa ansembe mogwirizana ndi dongosolo la tsiku ndi tsiku.+ Komanso anaika alonda a pazipata m’magulu awo kuti akhale m’zipata zosiyanasiyana+ chifukwa ndilo linali lamulo la Davide munthu wa Mulungu woona.

  • Yesaya 52:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tamvera! Alonda ako+ akufuula.+ Onse akufuula pamodzi mokondwera. Pamene Yehova azidzasonkhanitsanso okhala mu Ziyoni,+ iwo adzaona ndi maso awo.+

  • 1 Akorinto 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mulungu waika ziwalo zosiyanasiyana mumpingo.+ Choyamba atumwi,+ chachiwiri aneneri,+ chachitatu aphunzitsi,+ kenako ntchito zamphamvu,+ mphatso za kuchiritsa,+ utumiki wothandiza anthu,+ luso loyendetsa zinthu,+ ndi malilime osiyanasiyana.+

  • Aefeso 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo anapereka ena monga atumwi,+ ena monga aneneri,+ ena monga alaliki,*+ ena monga abusa ndi aphunzitsi,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena