1 Mbiri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri. 1 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.
17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri.
26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.