Ezara 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a alonda a pachipata, omwe anali ana a Salumu,+ ana a Ateri,+ ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita,+ ndi ana a Sobai, onse analipo 139.
42 Ana a alonda a pachipata, omwe anali ana a Salumu,+ ana a Ateri,+ ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita,+ ndi ana a Sobai, onse analipo 139.