Nehemiya 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ anali kulondera monga alonda a m’zipata.+ Amenewa anali kulondera pafupi ndi zipinda zosungiramo zinthu m’zipata za kachisi.
25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ anali kulondera monga alonda a m’zipata.+ Amenewa anali kulondera pafupi ndi zipinda zosungiramo zinthu m’zipata za kachisi.