Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri.

  • Ezara 2:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Ana a alonda a pachipata, omwe anali ana a Salumu,+ ana a Ateri,+ ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita,+ ndi ana a Sobai, onse analipo 139.

  • Nehemiya 7:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Alonda a pachipata,+ ana a Salumu,+ ana a Ateri, ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita, ana a Sobai,+ 138.

  • Nehemiya 11:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Alonda a pazipata+ anali Akubu, Talimoni,+ ndi abale awo amene anali kulondera m’zipata.+ Onse pamodzi analipo 172.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena