1 Mbiri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri. Nehemiya 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alonda a pazipata+ anali Akubu, Talimoni,+ ndi abale awo amene anali kulondera m’zipata.+ Onse pamodzi analipo 172.
17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri.
19 Alonda a pazipata+ anali Akubu, Talimoni,+ ndi abale awo amene anali kulondera m’zipata.+ Onse pamodzi analipo 172.