Nehemiya 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alonda a pazipata+ anali Akubu, Talimoni,+ ndi abale awo amene anali kulondera m’zipata.+ Onse pamodzi analipo 172.
19 Alonda a pazipata+ anali Akubu, Talimoni,+ ndi abale awo amene anali kulondera m’zipata.+ Onse pamodzi analipo 172.