1 Mbiri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri. Ezara 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a alonda a pachipata, omwe anali ana a Salumu,+ ana a Ateri,+ ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita,+ ndi ana a Sobai, onse analipo 139. Nehemiya 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ anali kulondera monga alonda a m’zipata.+ Amenewa anali kulondera pafupi ndi zipinda zosungiramo zinthu m’zipata za kachisi.
17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri.
42 Ana a alonda a pachipata, omwe anali ana a Salumu,+ ana a Ateri,+ ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita,+ ndi ana a Sobai, onse analipo 139.
25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ anali kulondera monga alonda a m’zipata.+ Amenewa anali kulondera pafupi ndi zipinda zosungiramo zinthu m’zipata za kachisi.