Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Onse amene anasankhidwa kuti akhale alonda a pamakomo analipo 212. Iwo anakhala m’midzi yawo+ mogwirizana ndi mndandanda wa mayina wotsatira makolo awo.+ Davide+ ndi Samueli wamasomphenya+ anaika amenewa pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo.+

  • 2 Mbiri 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho anaika alonda a pazipata+ pafupi ndi zipata+ za nyumba ya Yehova kuti aliyense wodetsedwa mwa njira ina iliyonse asalowe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena