1 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu. 1 Mbiri 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anachita maere+ ofanana kwa wamng’ono ndi wamkulu potsata nyumba za makolo awo,+ kuti apeze ogwira ntchito pachipata chilichonse.
26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.
13 Choncho anachita maere+ ofanana kwa wamng’ono ndi wamkulu potsata nyumba za makolo awo,+ kuti apeze ogwira ntchito pachipata chilichonse.