1 Mbiri 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Maere a kum’mawa anagwera Selemiya.+ Anachitanso maere a Zekariya+ mwana wake, yemwe anali phungu+ wanzeru, ndipo maere ake anali oti akhale kumpoto.+
14 Maere a kum’mawa anagwera Selemiya.+ Anachitanso maere a Zekariya+ mwana wake, yemwe anali phungu+ wanzeru, ndipo maere ake anali oti akhale kumpoto.+