1 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.
26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.