Nehemiya 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana aamuna a oimbawo anasonkhana pamodzi kuchokera m’Chigawo*+ chapafupi, m’madera onse ozungulira Yerusalemu komanso m’midzi yonse kumene Anetofa anali kukhala.+ Nehemiya 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ena anachokera ku Beti-giligala+ komanso m’dera la Geba+ ndi la Azimaveti,+ pakuti kumeneko kunali midzi+ imene oimba anamanga kuzungulira Yerusalemu yense.
28 Ana aamuna a oimbawo anasonkhana pamodzi kuchokera m’Chigawo*+ chapafupi, m’madera onse ozungulira Yerusalemu komanso m’midzi yonse kumene Anetofa anali kukhala.+
29 Ena anachokera ku Beti-giligala+ komanso m’dera la Geba+ ndi la Azimaveti,+ pakuti kumeneko kunali midzi+ imene oimba anamanga kuzungulira Yerusalemu yense.